Download M’manja Mwanu Mp3 by Beracah
Here’s an amazing song and music lyrics from the talented Malawian gospel musician, “Beracah“. It’s a song titled “M’manja Mwanu“, and was released in 2024. This beautiful song, accompanied by a stunning music video, audio, and lyrics, is sure to captivate listeners of all ages. Don’t miss out on this beautiful musical experience.
Get MP3 audio, Download, Stream, and Share this powerful song with your friends and family, and let the blessings overflow! By sharing it with your loved ones, you’re spreading the goodness and joy that this song brings. #CeeNaija
Download More BERACAH Songs Here
Lyrics: M’manja Mwanu by Beracah
Yense osambitsidwa ndi mwazi wa Yesu
Ndimwazi wa Yesu
Ali mmanja mwake
Palibe dzina lina lomwe ndingafune kutsata
Ndipo palibe kwina komwe ndingafune kukhala
Kuposa mwandiyikako kutsata mukuchitazo
Ufumu wanu ndilondola till the day that you return
Palibe chondikopa
Palibe chondisuntha
Mwa inu muli zonse
Author and the finisher
Ukulu wanu ndi osatha
Ufumu wanu wamuyaya
Chondilimbitsa you’re above it all and I’m so thankful
Tili m’manja mwanu
m’manja mwanu m’manja mwanu
Ndine wanu
Tili m’manja mwanu
m’manja mwanu
Ndine wanu m’manja mwanu
Mwanu mwanu (mwanu mwanu)
Mwanu mwanu (mwanu mwanu)
Mwanu mwanu (mwanu mwanu)
Mwanu mwanu yeah
Chikondi chanu ncholemera
Chindichotsa manyazi
Ndili kutali munabwera kundikokera nkati
Yesu my solid ground
No one can hold me down
No one can wear your crown
You’re so profound
Palibe chondikopa
Palibe chondisuntha
Mwa inu muli zonse
Author and the finisher
Ukulu wanu ndi osatha
Ufumu wanu wamuyaya
Chondilimbitsa you’re above it all and I’m so thankful
Tili m’manja mwanu
m’manja mwanu m’manja mwanu
Ndine wanu
Tili m’manja mwanu
m’manja mwanu
Ndine wanu m’manja mwanu
Mwanu mwanu (mwanu mwanu)
Mwanu mwanu (mwanu mwanu)
Mwanu mwanu (mwanu mwanu)
Mwanu mwanu yeah
Mwanu mwanu (mwanu mwanu)
Mwanu mwanu (mwanu mwanu)
Mwanu mwanu (mwanu mwanu)
Mwanu mwanu yeah
Yense osambitsidwa ndi mwazi wa Yesu
Ndimwazi wa yesu ndimwazi wa Yesu
Yense osambitsidwa ndi mwazi wa Yesu
Ndimwazi wa Yesu ali mmanja mwake