Download Linny Hoo Mp3 by Namadingo Ft. Giddes Chalamanda
Here’s a song by the African prolificย music artistย and talented singer and songwriter โNamadingoโ. Thisย songย is titled โLinny Hooโ featuring Giddes Chalamanda. You’ll surely enjoyย as you listen.
Get Audio Mp3, stream, share, and be blessed.
DOWNLOAD MORE NAMADINGO SONGS HERE
Lyrics: Linny Hoo by Namadingo
LINNY OOH
LINNY OOH
UYU LINNY LERO MWANA AMENEYU
MWANA WA NZERU
LINNY HOO
LINNY
LINNY HOO
UYU LINNY LERO MWANA AMENEYU MWANA WA NZERU
KUKACHAMA M’MAMA WA AAH AAH
AMATENG’A TCHACHE KUSETSA
PAKHOMO PAKHOMO PA MAYI WACHE
KUKACHA M’MAMAWA AAH AAH
EARLY MORNING
AMATENG’A TCHACHE KUSETSA
PAKHOMO PAKHOMO PA MAYI WACHE
MAKOLO A LINNY
ETI MAKOLO A LINNY
AMUYAMIKIRA
AKUTI LINNY LERO MWANA AMENEYU
MWANA WA NZERU
MAKOLO A LINNY
MAKOLO A LINNY
AMUYAMIKIRA
AKUTI LINNY LERO MWANA AMENEYU
MWANA WA NZERU
LINNY
LINNY HOO
LINNY HOO
LINNY HOO
UYU LINNY LERO MWANA AMENEYU
MWANA WA NZERU
Tintintile, oooh, tintintintitile, oooh, tintalintantanta, oooh, tantintintanta, ooooh
LINNY HOO
LINNY
LINNY HOO UYU LINNY LERO MWANA AMENEYU MWANA WA NZERU
A GIDE, GOGO WA NAMADINGO
AMUYAMIKIRA
AKUTI NAMADINGO MWANA AMENEYU MWANA WA NZERU
SIMIKUNAMANA AGOGO
NTHAWI ZINA INE
NDIMALOTA INE
BAMBO ANGA ATANDISIYA NDASALA NDEKHA
NTHAWI ZINA INE
NTHAWI ZINA INE
NDIMALOTA INE BAMBO ANGA ATAMWALIRA NDASALA NDEKHA
NKHONDO AMAMA (NKHONDO AMAMA)
NKHONDO AMAMA CHALAMANDA
OZAFERA MOYENDA WE
NKHONDO MAMA HII
NKHONDO UNE AMAMA WEE
NKHONDO AMAMA CHALAMANDA
UZAFERA MOYENDA WE
NDANG’OVYA MBIRIYO MBIRIYO
MBIRIYO MWAONA LERO
NDANG’OVYA MBIRIYO KA
MBIRIYO MBIRIYO MWAONA LERO
AGIDDES AYIMBA EEH
AYIMBA EEH
ZOKOMATU MWAONA LERO
NDIPO CHALAMANDA AYIMBA EEH
AYIMBA EEH
ZOKOMATU MWAONA LERO
NDAMVA KUTI MWAKWATIRA
MWABALA MWANA WOYERA
DZINA LAKE MUSOLO EEH
MUNAMVA KWA NDANI KUTI
MWAKWATIRA
NDAMVA KUTI MWAKWATIRA
MWABALA MWANA WOYERA
DZINA LAKE MUSOLO EEH
MNANGOPANGA UNKHOSWA UKWATI
NZAKUYITANARI
MUSOLO EEH
ETI MUSOLO EEH
MUSOLO EEH
MUSOLO MAYI
MUSOLO EEH
MUSOLO EEH
MUSOLO MAYI
MWANA AMENEYI NDI NAAYI AKE
NDIKUFUNA NDIPITE NAWO KU UK
MAPHUNZIRO ONSE ONSEE
AKAPHUZIRE KU UK
MAPHUNZIRO ONSE ONSEE
AKAPHUZURE KU UK
NDAMVA AGOGO NDAMVA
KOMA TIMIYEKO CHE MERI
CHE MERI KUNALI CHE MERI
CHE MERI UUHMMM
CHE MERI UUHMMM
CHE MERI KUNALI CHE MERI
CHE MERI MAMA MWE
IYA MERI MWE IYA DARLIE
KUNALI CHE MERI
HIIIYO IYA MERI MWE IYA DARLIE
KUNALI CHE MERI
TIMBIYEPO HAKOMA PAJA
HIIIYO IYA MERI MWE IYA DARLIE
KUNALI CHE MERI
AKAFUNA KUNENA NANE
AGIDDES AGIDDES AGIDDES AGIDDES
INU ABWANA TABWERANI KUNO
AKAFUNA KUNENA NANE
CHALAMANDA CHALAMANDA
CHALAMANDA CHALAMANDA INU
ABWANA TABWERANI KUNO
AKAFUNA KUNENA NANE
AGIDDES AGIDDES AGIDDES AGIDDES
INU ABWANA TABWERANI KUNO
ZINALI CHONCHO NTHAWI YA
NAPOLO
NAPOLO IIIH WACHABE
NAPOLO IIIH WACHABE
NAPOLO WACHABE
NAPOLO WACHABE
WATENGA INGALAMU, TENG’A ING’ALAMU
KUKATAYA KUMCHING’A
KUTUMA AKAIDI KUKATOLA
POBWERA ADONA NAHRA MAYIWE
WACHABE NAPOLO WACHABE
NAPOLO WACHABE
TIMALIZE NDI BUFFALO SOLDIER
BUFFALO SOLDIER
BUFFALO TO AMERICA
BUFFALO SOLDIER
BUFFALO TO AMERICA
WHEN I WAS A YOUNG BOY
I DREAMED.. TO THERE IN AMERICA
WHEN I WAS A YOUNG BOY NGATI INE KA YOUNG BOY
I DREAMED.. TO THERE IN AMERICA
OYIYOIYOIYO (X12)
IF I HAD MUCH MONEY
I GO TO SEE INI AMERICA
OOH YEAH
IF I HAD MUCH MONEY I GO TO SEE INI AMERICA